Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 10/08 tsamba 12-31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
  • Galamukani!—2008
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Zinachitikira Kuti?
  • Kuchokera M’magazini Ino
  • Zithunzi Zoti Ana Apeze
  • Ndani Ali M’gulu la Makolo a Yesu?
  • MAYANKHO A MAFUNSO A PATSAMBA 31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2008
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2008
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2008
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2008
Onani Zambiri
Galamukani!—2008
g 10/08 tsamba 12-31

Kodi Mungayankhe Bwanji?

Zinachitikira Kuti?

1. Kodi ndi mumtsinje uti umene Mose akadali khanda anamupeza?

ZOKUTHANDIZANI: Werengani Eksodo 2:1-10.

Pamapu awa lembani mzere wozungulira yankho lanu.

Firate

Yordano

Nile

◼ Kodi ndani amene ankayang’anira Mose ataima chapatali?

․․․․․

◼ Kodi ndani amene anapeza Mose akuyandama mumtsinje?

․․․․․

◼ Kodi ndani anasankhidwa kuti azilera Mose?

․․․․․

KAMBIRANANI:

Kodi mlongo wa Mose anasonyeza makhalidwe otani? Ngati muli ndi m’bale kapena mlongo wanu, kodi mungamutsanzire bwanji mlongo wa Mose?

Kuchokera M’magazini Ino

Yankhani mafunsowa, ndipo lembani vesi kapena mavesi a m’Baibulo omwe akusowa.

TSAMBA 8 Kodi munthu aliyense wochenjera amatani? Miyambo 13:․․․․․

TSAMBA 8 Kodi chingachitike n’chiyani mukamakhala panokha? Miyambo 18:․․․․․

TSAMBA 9 Kodi mayi wabwino amatani? Miyambo 31:․․․․․

TSAMBA 9 N’chifukwa chiyani muyenera kuyesetsa kukhala ndi luso la kulingalira? Miyambo 2:․․․․․

Zithunzi Zoti Ana Apeze

Kodi mungapeze zithunzi izi m’magazini ino? Fotokozani zimene zikuchitika pa chithunzi chilichonse.

Ndani Ali M’gulu la Makolo a Yesu?

Onani zokuthandizani kupeza yankho. Onaninso malembawo. Kenaka lembani mayina olondola pa mizereyi.

2. ․․․․․

ZOKUTHANDIZANI: Ndinakanthidwa ndi khate chifukwa ndinafuna kupereka nsembe yofukiza paguwa la nsembe la Yehova.

Werengani 2 Mbiri 26:16-19.

3. ․․․․․

ZOKUTHANDIZANI: Ndinali mfumu yabwino ndipo ndinamanga chipata cha kumtunda cha nyumba ya Yehova.

Werengani 2 Mbiri 27:1-4.

4. ․․․․․

ZOKUTHANDIZANI: Ndinapsereza ana anga nsembe m’Chigwa cha Hinomu.

Werengani 2 Mbiri 28:1, 3, 4.

◼ Mayankho ali pa tsamba 12

MAYANKHO A MAFUNSO A PATSAMBA 31

1. Nile.

◼ Mlongo wa Mose.

◼ Mwana wamkazi wa Farao.

◼ Mayi a Mose.

2. Uziya.—Mateyo 1:8.

3. Yotamu.—Mateyo 1:9.

4. Ahazi.—Mateyo 1:9.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena