Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 12/08 tsamba 14-31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
  • Galamukani!—2008
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Zinachitikira Kuti?
  • Kuchokera M’magazini Ino
  • Zithunzi Zoti Ana Apeze
  • Ndani Ali M’gulu la Makolo a Yesu?
  • MAYANKHO A MAFUNSO A PA TSAMBA 31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2008
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2008
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2008
  • Zoti Banja Likambirane
    Galamukani!—2010
Onani Zambiri
Galamukani!—2008
g 12/08 tsamba 14-31

Kodi Mungayankhe Bwanji?

Kodi Zinachitikira Kuti?

1. Kodi Yesu ananyamukira kuti popita kumwamba?

ZOKUTHANDIZANI: Werengani Machitidwe 1:6-12.

Lembani mzere wozungulira yankho lanu pamapupo.

Phiri la Karimeli

Phiri la Gerizimu

Phiri la Maolivi

Hebroni

◼ Yesu atatsala pang’ono kupita kumwamba, ophunzira ake anamufunsa chiyani?

․․․․․

◼ Kodi Yesu anati ophunzira ake adzatani?

․․․․․

KAMBIRANANI:

Kodi mawu a angelo a pa Machitidwe 1:11 akwaniritsidwa bwanji? Kodi mungatani kuti muzichita nawo ntchito imene Yesu anauza otsatira ake, monga momwe zalembedwera pa Machitidwe 1:8?

Kuchokera M’magazini Ino

Yankhani mafunsowa, ndipo lembani vesi kapena mavesi a m’Baibulo omwe akusowapo.

TSAMBA 4 Kodi Baibulo limanena chiyani za Eliya? Yakobe 5:․․․

TSAMBA 7 Kodi munthu amakhala ndi moyo ndi chiyani? Mateyo 4:․․․

TSAMBA 19 Kodi ndani amapambana mbale kuumirira? Miyambo 18:․․․

TSAMBA 20 Kodi pali nthawi yochita chiyani? Mlaliki 3:․․․

Zithunzi Zoti Ana Apeze

Kodi mungapeze zithunzi izi m’magazini ino? Fotokozani zimene zikuchitika pa chithunzi chilichonse.

Ndani Ali M’gulu la Makolo a Yesu?

Onani zokuthandizani kupeza yankho. Onaninso malembawo. Kenaka lembani mayina olondola pa mizereyi.

2. ․․․․․

ZOKUTHANDIZANI: Panthawi ya ulamuliro wanga, Hilikiya “anapeza buku la chilamulo la Yehova mwa dzanja la Mose.”

Werengani 2 Mbiri 34:1, 14.

3. ․․․․․

ZOKUTHANDIZANI: Ndinali chiwanga kapena kuti kazembe woyamba wa Ayuda amene anabwerera ku Isiraeli kuchoka ku Babulo.

Werengani Hagai 1:14.

4. ․․․․․

ZOKUTHANDIZANI: Ntchito yanga inali yopala matabwa.

Werengani Mateyo 1:16; 13:55.

◼ Mayankho ali pa tsamba 14

MAYANKHO A MAFUNSO A PA TSAMBA 31

1. Phiri la Maolivi.

◼ Anamufunsa Yesu nthawi imene adzabwezeretse Ufumu.

◼ Yesu anati ophunzira ake adzalalikira za iye mpaka kumalekezero a dziko lapansi.

2. Yosiya.​—Mateyo 1:⁠10.

3. Zerubabele.​—Mateyo 1:⁠12.

4. Yosefe.​—Mateyo 1:⁠16.

[Mawu a Chithunzi patsamba 31]

Center circle: Oxford Scientific/​photolibrary

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena