Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 6/11 tsamba 32
  • Kodi Mukufuna Kulimvetsa Baibulo?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mukufuna Kulimvetsa Baibulo?
  • Galamukani!—2011
Galamukani!—2011
g 6/11 tsamba 32

Kodi Mukufuna Kulimvetsa Baibulo?

● Anthu mamiliyoni ambiri ayamba kumvetsa zimene Baibulo limanena, pophunzira buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? Bukuli lili ndi mitu 19 ndipo mitu ina ndi yakuti:

“Kodi Zoona Zenizeni za Mulungu N’zotani?”

“Kodi Yesu Kristu Ndani?”

“Kodi Akufa Ali Kuti?”

“Kodi Tili ‘M’masiku Otsiriza’?”

“N’chifukwa Chiyani Mulungu Amalola Kuti Anthu Azivutika?”

“Zimene Mungachite Kuti Banja Lanu Likhale ndi Moyo Wosangalala”

Mukhoza kupempha kuti munthu aziphunzira nanu Baibulo. Mukhozanso kuitanitsa bukuli polemba adiresi yanu m’mizere ili m’munsiyi, ndipo tumizani ku adiresi yoyenera yomwe ili patsamba 5 m’magazini ino.

□ Ndikupempha kuti munditumizire bukuli.

□ Nditumizireni munthu kuti ayambe kuphunzira nane Baibulo kwaulere.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena