BOKOSI 5A
“Iwe Mwana Wa Munthu, Kodi Waona Zimenezi?”
Losindikizidwa
Zinthu 4 zonyansa kwambiri zimene Ezekieli anaona m’bwalo la mkati la kachisi. (Ezek. 8:5-16)
1. FANO LOIMIRA NSANJE
2. AKULUAKULU 70 AKUPEREKA NSEMBE ZOFUKIZA KWA MILUNGU YABODZA
3. ‘AZIMAYI AKULIRIRA MULUNGU WOTCHEDWA TAMUZI’
4. AMUNA 25 ‘AKUGWADIRA DZUWA’