Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • rr tsamba 131
  • Kuphatikiza Ndodo Ziwiri

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kuphatikiza Ndodo Ziwiri
  • Yehova Wabwezeretsa Kulambira Koyera
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • “ndodo ya Yuda”
  • “ndodo ya Yosefe yoimira Efuraimu”
  • “zikhale ndodo imodzi mʼdzanja lako”
  • Mafunso Ochokera kwa Owerenga
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2016
  • “Ndidzawachititsa Kuti Akhale Mtundu Umodzi”
    Yehova Wabwezeretsa Kulambira Koyera
  • Kamtengo Kamene Kamayeretsa Mano
    Galamukani!—2003
Yehova Wabwezeretsa Kulambira Koyera
rr tsamba 131

BOKOSI 12A

Kuphatikiza ndodo Ziwiri

Losindikizidwa

Yehova anauza Ezekieli kuti alembe pa ndodo imodzi kuti “ndodo ya Yuda” komanso pa ndodo ina alembe kuti “ndodo ya Yosefe yoimira Efuraimu.”

Ndodo ziwiri za ulosi wa Ezekieli.

“ndodo ya Yuda”

KALE

Ufumu wa Yuda wa mafuko awiri

MASIKU ANO

Odzozedwa

“ndodo ya Yosefe yoimira Efuraimu”

KALE

Ufumu wa Isiraeli wa mafuko 10

MASIKU ANO

Nkhosa zina

Ezekieli wagwira ndodo ziwiri m’dzanja limodzi.

“zikhale ndodo imodzi mʼdzanja lako”

KALE

537 B.C.E. Anthu amene ankalambira Mulungu woona anabwera kuchokera m’mitundu yosiyanasiyana, anamanganso Yerusalemu ndipo anayamba kulambira Yehova monga mtundu umodzi.

MASIKU ANO

Kuyambira mu 1919, anthu a Mulungu pang’ono ndi pang’ono akugwirizananso kuti azitumikira Mulungu ngati “gulu limodzi.”

Mfundo yaikulu ndi yokhudza mgwirizano

Ulosiwu sukufotokoza kuti panali ndodo imodzi imene inathyoledwa n’kukhala ndodo ziwiri kenako n’kuzilumikiza kukhalanso ndodo imodzi. Koma ukunena za ndodo ziwiri zimene zinaphatikizidwa n’kukhala ndodo imodzi. Choncho ulosiwu sukufotokoza kwambiri zimene zinachitika kuti mtundu wa Isiraeli ugawanike n’kukhala maufumu awiri. Koma ukufotokoza zimene zinachitika kuti maufumu awiriwo akhale ufumu umodzi.

Bwererani ku mutu 12, onani ndime 3-6, 13, 14

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena