Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • scl tsamba 15-16
  • Anthu Ocheza Nawo

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Anthu Ocheza Nawo
  • Malemba Othandiza pa Moyo wa Chikhristu
Malemba Othandiza pa Moyo wa Chikhristu
scl tsamba 15-16

Anthu Ocheza Nawo

Kodi anthu ofunika kwambiri omwe munthu angamacheze nawo ndi ati?

Sl 25:14; Yoh 15:13-15; Yak 2:23

Onaninso Miy 3:32

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Ge 5:22-24​—Inoki anali pa ubwenzi wolimba ndi Mulungu

    • Ge 6:9​—Nowa anayenda ndi Mulungu mofanana ndi agogo ake a Inoki

N’chifukwa chiyani timafunikira mabwenzi abwino?

Miy 13:20; 17:17; 18:24; 27:17

Onaninso Miy 18:1

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Ru 1:16, 17​—Rute anasonyeza kuti anali mnzake wapamtima wa Naomi

    • 1Sa 18:1; 19:2, 4​—Yonatani ndi Davide anali mabwenzi apamtima

    • 2Mf 2:2, 4, 6​—Elisa anasonyeza chikondi chokhulupirika kwa mneneri Eliya

N’chifukwa chiyani tiyenera kumasonkhana nthawi zonse ndi Akhristu anzathu?

Aro 1:11, 12; Ahe 10:24, 25

Onaninso Sl 119:63; 133:1; Miy 27:9; Mac 1:13, 14; 1At 5:11

Kodi mungatani kuti mupeze anzanu abwino komanso kuti inuyo mukhale bwenzi labwino kwa ena?

Lu 6:31; 2Ak 6:12, 13; Afi 2:3, 4

Onaninso Aro 12:10; Aef 4:31, 32

Kodi ndi mavuto ena ati amene tingakumane nawo chifukwa chocheza ndi anthu omwe sakonda Yehova?

Miy 13:20; 1Ak 15:33; Aef 5:6-9

Onaninso 1Pe 4:3-5; 1Yo 2:15-17

Onaninso “Kukonda Dziko”

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Ge 34:1, 2​—Dina anakumana ndi mavuto chifukwa chosankha kucheza ndi anthu oipa

    • 2Mb 18:1-3; 19:1, 2:​—Yehova anauza Yehosafati yemwe anali mfumu yabwino, kuti asachite mgwirizano ndi Ahabu yemwe anali mfumu yoipa

Kodi tiyenera kupewa kumacheza ndi aliyense amene satumikira Yehova Mulungu?

Mt 28:19, 20; Yoh 17:15, 16; 1Ak 5:9, 10

N’chifukwa chiyani n’kulakwa kukwatirana ndi munthu yemwe sanadzipereke kwa Yehova komanso kubatizidwa?

Onani “Ukwati”

N’chifukwa chiyani tiyenera kupewa kumacheza ndi anthu omwe anachotsedwa mumpingo wa Chikhristu?

Aro 16:17; 1Ak 5:11; 2Yo 10, 11

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena