Zosangalatsa
Kodi n’kulakwa kuti Akhristu azichita zosangalatsa?
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
Mko 6:31, 32—Ngakhale kuti anali wotanganidwa, Yesu anawalimbikitsa ophunzira ake kuti apeze malo abwino kuti apume
Ndi mfundo ziti zomwe zingatithandize kuti tisamalole zosangalatsa kutisokoneza kuchita zinthu zauzimu?
Mt 6:21, 33; Aef 5:15-17; Afi 1:9, 10; 1Ti 4:8
Onaninso Miy 21:17; Mla 7:4