Dyera
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
Nu 11:4, 5, 31-33—Aisiraeli anali ndi dyera ndipo anagwira zinziri zochuluka kwambiri moti Yehova anawalanga chifukwa cha dyera lawolo
2Mf 5:20-27—Chifukwa cha dyera, Gehazi ananama kuti watumidwa ndi mneneri wa Yehova ndipo Yehova anamulanga chifukwa cha zimene anachitazi