Chinyengo 2Ak 6:4, 6; Yak 3:17 Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni: Mt 23:7, 23-28—Yesu anadzudzula atsogoleri achipembedzo chifukwa cha zochita zawo zachinyengo Aga 2:11-14—Mtumwi Paulo anadzudzula mtumwi Petulo chifukwa chochita zachiphamaso