Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2013
Wosonyeza deti la magazini imene muli nkhaniyo
BAIBULO
BAIBULO LIMASINTHA ANTHU
MAFUNSO OCHOKERA KWA OWERENGA
‘Analalikira kwa Mizimu Imene Inali M’ndende’ (1Pet. 3:19), 6/15
Kodi makolo azikhala ndi mwana wochotsedwa pa misonkhano? 8/15
N’chifukwa chiyani Yesu anagwetsa misozi? (Yoh. 11:35), 9/15
MBIRI YA MOYO WANGA
Ndinadalitsidwa Chifukwa Chomvera Yehova (E. Piccioli), 6/15
Tachita Utumiki wa Nthawi Zonse kwa Zaka 50 Kumpoto (A. and A. Mattila), 4/15
Timasangalala Kutumikira Yehova Kulikonse (M. and J. Hartlief), 7/15
MBONI ZA YEHOVA
MOYO NDI MAKHALIDWE ACHIKHRISTU
NKHANI ZOPHUNZIRA
Akulu Achikhristu Ndi Antchito Anzathu Otipatsa Chimwemwe,’ 1/15
Chilengedwe Chimatithandiza Kukhulupirira Kwambiri Mulungu, 10/15
Kodi Abusa 7 ndi Atsogoleri 8 Akuimira Ndani Masiku Ano, 11/15
Kodi Tikuphunzira Chiyani pa Pemphero Limene Linakonzedwa Bwino? 10/15
Kodi Timayamikira Cholowa Chathu Chochokera kwa Mulungu? 2/15
Mawu a Mulungu Azikuthandizani Ndipo Muzithandiza Nawo Ena, 4/15
Musalole Chilichonse Kukulepheretsani Kupeza Ulemerero, 2/15
Musalole Chilichonse Kusokoneza Ubwenzi Wanu ndi Yehova, 1/15
Muzisankha Zinthu Mwanzeru Kuti Musataye Madalitso Anu, 5/15
“Muzitsimikizira Kuti Zinthu Zofunika Kwambiri Ndi Ziti,” 4/15
“Ndani Kwenikweni Amene Ali Kapolo Wokhulupirika ndi Wanzeru?” 7/15
Popeza “Mwadziwa Mulungu” Kodi Muyenera Kuchita Chiyani? 3/15