Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • ijwfq nkhani 13
  • Kodi a Mboni za Yehova Ali ndi Abusa Amene Amalipidwa?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi a Mboni za Yehova Ali ndi Abusa Amene Amalipidwa?
  • Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Abusa Ndi Apamwamba Kuposa Anthu Ena Mumpingo?
    Galamukani!—2009
  • Kakonzedwe ka Mboni za Yehova
    Kodi Mulungu Amafunanji kwa Ife?
  • Kodi Nchifukwa Ninji Mboni Zimapitirizabe Kufikira Anthu?
    Nsanja ya Olonda—1994
  • Kodi Atumiki a Mulungu Ndani Lerolino?
    Nsanja ya Olonda—2000
Onani Zambiri
Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri
ijwfq nkhani 13
Mkhristu wa Mboni akuphunzitsa pogwiritsa ntchito Baibulo

Kodi a Mboni za Yehova Ali ndi Abusa Amene Amalipidwa?

Potsatira chitsanzo cha Akhristu a m’nthawi ya atumwi, m’gulu la Mboni za Yehova simukhala anthu ena amene amaonedwa kuti ndi apamwamba monga abusa. Akhristu onse obatizidwa amakhala odzipereka ndipo amagwira nawo ntchito yolalikira ndiponso kuphunzitsa anthu mawu a Mulungu. Mpingo uliwonse wa Mboni za Yehova umakhala ndi anthu pafupifupi 100. Mumpingo uliwonse mumakhala amuna odziwa bwino Baibulo ndipo amatumikira monga “akulu.” (Tito 1:5) Ndipo iwo salipidwa chifukwa cha utumiki wawo.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena