Limbitsani Cikhulupililo Canu!
AHEBERI 10:39
M’MAŴA
8:40 Nyimbo Zamalimba
8:50 Nyimbo Na. 119 na Pemphelo
9:00 N’cifukwa Ciani Tiyenela Kulimbitsa Cikhulupililo Cathu Pali Pano?
9:15 Kodi Mukuona “Wosaonekayo”?
9:30 “Munthu Amakhala Ndi Cikhulupililo Cifukwa ca Zimene Wamva”
9:55 Nyimbo Na. 104 na Zilengezo
10:05 “Makhalidwe Amene Mzimu Woyela Umatulutsa Ndiwo, . . . Cikhulupililo”
10:35 Kudzipatulila na Ubatizo
11:05 Nyimbo Na. 50
MASANA
12:20 Nyimbo Zamalimba
12:30 Nyimbo Na. 3
12:35 Zocitika
12:45 Cidule ca Nsanja ya Mlonda
13:15 Yosiilana: Thandizani Ena Kulimbitsa Cikhulupililo Cawo
• Thandizani Mwana Wanu Wacicepele
• Thandizani Wophunzila Baibo Wanu
• Thandizani Alambili Anzanu
14:00 Nyimbo Na. 38 na Zilengezo
14:10 ‘Yang’anitsitsani Mtumiki Wamkulu ndi Wokwanilitsa Cikhulupililo Cathu’
14:55 Nyimbo Na. 126 na Pemphelo