Zamkati
April 1, 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
NKHANI ZOPHUNZILA
JUNE 2-8, 2014
Tsanzilani Cikhulupililo ca Mose
TSAMBA 7 • NYIMBO: 33, 133
JUNE 9-15, 2014
TSAMBA 12 • NYIMBO: 81, 132
JUNE 16-22, 2014
Palibe Munthu Angatumikile Ambuye Aŵili
TSAMBA 17 • NYIMBO: 62, 106
JUNE 23-29, 2014
Limbani Mtima, Yehova Ndi Mtandizi Wanu
TSAMBA 22 • NYIMBO: 22, 95
JUNE 30, 2014–JULY 6, 2014
Kodi Mumayamikila Cisamalilo Cacikondi ca Yehova?
TSAMBA 27 • NYIMBO: 69, 120
NKHANI ZOPHUNZILA
▪ Tsanzilani Cikhulupililo ca Mose
▪ Kodi Mumaona “Wosaonekayo”?
Cifukwa ca cikhulupililo, Mose anaona zimene maso aumunthu sangaone. Nkhani izi zidzafotokoza mmene tingakhalile ndi cikhulupililo monga ca Mose ndi mmene ‘tingapitilizile kupilila moleza mtima ngati kuti tikuona Wosaonekayo.’—Aheb. 11:27.
▪ Palibe Munthu Angatumikile Ambuye Aŵili
▪ Limbani Mtima, Yehova Ndi Mtandizi Wanu
Anthu ambili amapita ku maiko ena kukafunafuna nchito. Ambili amasiya anzao a m’cikwati ndi ana. Nkhani izi zidzafotokoza zimene Yehova afuna kuti mitu ya mabanja izicita posamalila mabanja ao ndi mmene Yehova amawathandizila kucita zimenezo.
▪ Kodi Mumayamikila Cisamalilo Cacikondi ca Yehova?
Tikaŵelenga lemba limene limanena kuti “maso a Yehova ali paliponse,” ena a ife tingaganize kuti Yehova amatiyang’ana kuti aone ngati tiphwanya malamulo ake. Zimenezi zingacititse kuti tizimuopa. (Miy. 15:3) Koma m’nkhani ino tidzakambilana njila 5 zimene zionetsa mmene Yehova amatisamalila mwacikondi.
NKHANI ZINA M’MAGAZINI INO
N’cifukwa Ciani Anthu Amapemphela? 3