Zamkati
May 1, 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
NKHANI ZOPHUNZILA
JULY 7-13, 2014
Mmene ‘Tingayankhile Munthu Wina Aliyense’
TSAMBA 8 • NYIMBO: 96, 93
JULY 14-20, 2014
Muzionetsa Khalidwe Lopambana mu Ulaliki
TSAMBA 13 • NYIMBO: 73, 98
JULY 21-27, 2014
Yehova Ndi Mulungu Wadongosolo
TSAMBA 18 • NYIMBO: 125, 53
JULY 28, 2014–AUGUST 3, 2014
Kodi Mumayendela Limodzi ndi Gulu la Yehova?
TSAMBA 23 • NYIMBO: 45, 27
NKHANI ZOPHUNZILA
▪ Mmene ‘Tingayankhile Munthu Wina Aliyense’
▪ Muzionetsa Khalidwe Lopambana mu Ulaliki
Nthawi zina tikapita mu ulaliki timakumana ndi mafunso ovuta. Nkhani ziŵili zoyambilila zophunzila zifotokoza njila zitatu zimene tingagwilitsile nchito kuti tizipeleka mayankho ogwila mtima. (Akol. 4:6) Nkhani yaciŵili ionetsa mmene kutsatila mau a Yesu a pa Mateyu 7:12 kungatithandizile polalikila.
▪ Yehova Ndi Mulungu Wadongosolo
▪ Kodi Mumayendela Limodzi ndi Gulu la Yehova?
Yehova wakhazikitsa atumiki ake kuyambila nthawi zakale. M’nkhani ziŵilizi, tidzaphunzila zimene Mulungu afuna kuti tizicita monga anthu ake. Tidzaphunzilanso cifukwa cake tiyenela kukhala okhulupilika ku gulu limene Yehova amagwilitsila nchito masiku ano.
NKHANI ZINA M’MAGAZINI INO
Zimene Ena Amalosela Zimacitika, Koma Zambili Sizimacitika 3
Kodi Ndani Amadziŵadi Zamtsogolo? 4
Kuceza ndi Mnzathu—Kodi Mboni za Yehova Zimakhulupilila Yesu? 28