Zamkati
July 15, 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
YOPHUNZILA
SEPTEMBER 1-7, 2014
TSAMBA 7 • NYIMBO: 63, 66
SEPTEMBER 8-14, 2014
Anthu a Yehova “Aleke Kucita Zosalungama”
TSAMBA 12 • NYIMBO: 64, 61
SEPTEMBER 15-21, 2014
TSAMBA 23 • NYIMBO: 31, 92
SEPTEMBER 22-28, 2014
TSAMBA 28 • NYIMBO: 102, 103
NKHANI ZOPHUNZILA
▪ “Yehova Amadziŵa Anthu Ake”
▪ Anthu a Yehova “Aleke Kucita Zosalungama”
Nkhani zimenezi zidzatithandiza kumvetsetsa lemba la 2 Timoteyo 2:19, ndipo zionetsa kuti lembali limagwilizana ndi zocitika za m’nthawi ya Mose. Tidzaphunzila mmene Akristu masiku ano, angaonetsele kuti ‘amadziŵika ndi Yehova,’ ndi kuti ‘aleka kucita zosalungama.’
▪ “Inu Ndinu Mboni Zanga”
▪ “Mudzakhala Mboni Zanga”
M’nkhanizi, tidzakambilana kufunika kokhala ndi dzina lakuti Mboni za Yehova. Tidzaphunzila kuti kunyadila nchito yocitila umboni za Yehova ndi Yesu kumafuna kuti tikhale acangu mu ulaliki. Kumafunanso kuti tizilemekeza Mulungu ndi Kristu ndi khalidwe lathu bwino.
NKHANI ZINA M’MAGAZINI INO
CIKUTO: Alongo aŵili agwilitsila nchito buku la Zimene Baibo Imaphunzitsa M’ceni-ceni, polalikila kwa azimai aŵili acindebele amene avala zovala zacindebele. Iwo akhala patsogolo pa nyumba ya kamangidwe ka kumudzi wacindebele. Andebele ndi ocepa ku South Africa, ali cabe ciŵelengelo ca 2 pelesenti
SOUTH AFRICA
KULI ANTHU
50,500,000
OFALITSA ONSE
94,101
OFALITSA ACINDEBELE
1,003