Zamkati
July 15, 2015
© 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
YOPHUNZILA
AUGUST 31, 2015–SEPTEMBER 6, 2015
Thandizani Kukongoletsa Paladaiso Wauzimu
TSAMBA 7
SEPTEMBER 7-13, 2015
“Cipulumutso Canu Cikuyandikila”
TSAMBA 14
SEPTEMBER 14-20, 2015
Khalanibe Okhulupilika ku Ufumu wa Mulungu
TSAMBA 22
SEPTEMBER 21-27, 2015
TSAMBA 27
NKHANI ZOPHUNZILA
▪ Thandizani Kukongoletsa Paladaiso Wauzimu
Anthu a Yehova akusangalala ndi paladaiso wauzimu amene ali m’mbali ya padziko lapansi ya gulu la Mulungu. Kodi tingasonyeze bwanji kuti timayamikila mphatso imeneyi yocokela kwa Yehova? Nanga aliyense wa ife angacite ciani kuti athandize kukongoletsa paladaiso ameneyu? Nkhaniyi iyankha mafunso amenewa.
▪ “Cipulumutso Canu Cikuyandikila”
Nkhaniyi ikufotokoza zinthu zabwino zimene tikuyembekezela posacedwapa. Ifotokozanso cifukwa cake tifunika kukhulupilila kuti Yehova adzatipulumutsa pa cisautso cacikulu.
▪ Khalanibe Okhulupilika ku Ufumu wa Mulungu
M’dziko la Satanali anthu ambili ndi okhulupilika ku dziko lao, fuko lao, ndi cikhalidwe cao. Koma, ife tinalonjeza Yehova kuti tidzakhala okhulupilika kwa iye. Nkhaniyi ifotokoza bwino cifukwa cake sititengamo mbali m’mikangano ya dzikoli ndiponso mmene tingaphunzitsile maganizo athu ndi cikumbumtima cathu kuti tisamatengemo mbali m’mikangano imeneyi.
▪ Awa Ndi Malo Athu Olambilila
Anthu a Yehova amakumana kuti alambile Mulungu mu Nyumba za Ufumu ndi malo ena masauzande ambilimbili padziko lonse lapansi. M’nkhaniyi tikambilana mfundo za m’Malemba zimene zidzatilimbikitsa kulemekeza malo amenewa ndi kupelekela ndalama zocilikizila nchito yomanga nyumbazi. Tikambilananso mmene tingasamalile malo amenewa kuti azipeleka ulemelelo kwa Yehova.
NKHANI ZINA M’MAGAZINI INO
3 Anadzipeleka Mofunitsitsa—ku Russia
PACIKUTO: Abale ndi alongo akudya cakudya ca masana pambuyo polalikila cigawo ca m’mawa ku madela a ku Siberia
KU RUSSIA
KULI ANTHU
143,930,000
OFALITSA