Yophunzila
AUGUST 2017
NKHANI ZOPHUNZILA: SEPTEMBER 25–OCTOBER 22, 2017
© 2017 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PIKICA YA PACIKUTO:
NETHERLANDS
Apainiya aŵili ku Amsterdam akulalikila uthenga wa Ufumu kwa munthu wopita m’njila
OFALITSA
29,839
MAPHUNZILO A BAIBO
12,802
OPEZEKA PA CIKUMBUTSO (2016)
51,404
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Ndalama zoyendetsela nchitoyi n’zimene anthu amapeleka mwa kufuna kwawo.
Ngati mufuna kupeleka ndalama zothandizila nchitoyi, yendani pa www.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.