Zamkati
WIKI YA JANUARY 29, 2018–FEBRUARY 4, 2018
WIKI YA FEBRUARY 5-11, 2018
8 “Ine Ndili Ndi Ciyembekezo mwa Mulungu”
Ni zocitika zakale ziti zimene zinathandiza Akhristu kukhala na cikhulupililo cakuti akufa adzauka? Nanga kuganizila zocitika zimenezo komanso ciyembekezo cimene anthu ena okhulupilika akale anali naco, kuyenela kukhudza bwanji ciyembekezo canu? Nkhani zimenezi zidzalimbitsa cikhulupililo canu cakuti akufa adzauka.
14 Mafunso Ocokela kwa Oŵelenga
16 Mafunso Ocokela kwa Oŵelenga
WIKI YA FEBRUARY 12-18, 2018
18 Makolo—Thandizani Ana Anu Kupeza ‘Nzelu Zowathandiza Kuti Akapulumuke’
WIKI YA FEBRUARY 19-25, 2018
23 Acicepele—“Pitilizani Kukonza Cipulumutso Canu”
Anthu masauzande ambili amabatizika caka ciliconse. Ena mwa anthu amenewa ni acicepele. Kubatizika kumatsegula mwayi wolandila madalitso ambili, koma kumabweletsanso udindo. Makolo, kodi mungawathandize bwanji ana anu kukonzekela ubatizo? Ngati ndinu wacicepele wobatizika kapena amene mufuna kudzabatizika, kodi mungalimbitse bwanji ubwenzi wanu na Yehova?
28 Mbili Yanga—N’nasiya Zinthu Zina Pofuna Kutsatila Ambuye