LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • wp19 na. 2 tsa. 16
  • Iye “Amakudelani Nkhawa”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Iye “Amakudelani Nkhawa”
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2019
  • Nkhani Zofanana
  • Mungakhale pa Ubwenzi na Mulungu
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2019
  • Mmene Coonadi Cingakuthandizileni
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2020
  • Kodi Mulungu amamvela bwanji akaona kuti muvutika?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2018
  • Kodi Mavuto Adzathadi?
    Kodi Mavuto Adzathadi?
Onaninso Zina
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2019
wp19 na. 2 tsa. 16

Iye “Amakudelani Nkhawa”

Mkazi wacitsikana amwetulila, ndipo ayenda mokondwela mumsewu wopita anthu ambili

Ngakhale kuti ena angakusiyeni panthawi ya mavuto, pali wina wake amene sangakusiyeni. Kodi ndani ameneyo?

Mfumu yakale Davide inati: “Ngakhale bambo anga ndi mayi anga atandisiya, Yehova adzanditenga.”—Salimo 27:10.

Yehova ni “Tate wacifundo cacikulu ndi Mulungu amene amatitonthoza m’njila iliyonse, amenenso amatitonthoza m’masautso athu onse.”—2 Akorinto 1: 3,4.

‘Mutulileni nkhawa zanu zonse, pakuti amakudelani nkhawa.’—1 Petulo 5:7.

Kuti mudziŵe mmene Mulungu angakusamalileni, onani phunzilo 8 m’buku lakuti, Kondwelani Na Moyo Kwamuyaya!, lolembedwa na Mboni za Yehova. Limapezekanso pa webusaiti ya www.jw.org

Kuti mudziŵe zambili za mmene mungakhalile bwenzi la Mulungu, onani phunzilo 8 m’bukuli, Kondwelani Na Moyo Kwamuyaya!, lopangidwa na Mboni za Yehova, ndipo limapezekanso pa www.jw.org

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani