Ndandanda ya Mlungu wa October 8
MLUNGU WA OCTOBER 8
Nyimbo 75 ndi Pemphelo
□ Phunzilo la Baibo la Mpingo:
bt mutu 13 ndime 8-16, bokosi pa tsa. 105 (Mph. 30)
□ Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibo: Danieli 7-9 (Mph. 10)
Na. 1: Danieli 7:13-22 (Mph. 4 kapena zocepelapo)
Na. 2: Kodi Baibo Imasonyeza Kuti Akristu Oona Adzalinganizidwa Kukhala Gulu?—rs tsa. 141 ndime 2-tsa. 142 ndime 2 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Yehova ndi Wokhulupilika M’njila Zanji?—Chiv. 15:4; 16:5 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Nchito:
Nyimbo 133
Mph. 10: Ngati munthu akamba kuti, ‘Ndine Wotangwanika’ Kukambilana kozikidwa pa buku la Kukambitsirana, tsamba 19, ndime 5, mpaka tsamba 20 ndime 4. Kambilanani mayankhidwe ena amene apelekedwa m’bukuli ndi ena omwe agwilitsidwapo nchito mogwila mtima m’gawo lanu. Khalani ndi zitsanzo ziŵili zacidule.
Mph. 10: Tiphunzilapo Ciani? Kukambilana. Malemba awa aŵelengedwe: Mateyu 21:12-16 ndi Luka 21:1-4. Kambilanani zimene tiphunzilapo pa Malembawa.
Mph. 10: “Kodi Mukhoza Kumacitako Ulaliki wa M’madzulo?” Mafunso ndi mayankho. Pokambilana ndime 2, pemphani omvela kuti asimbe zocitika zimene anasangalala nazo muulaliki wa m’madzulo.
Nyimbo 92 ndi Pemphelo