Ndandanda ya Mlungu wa November 19
MLUNGU WA NOVEMBER 19
Nyimbo 81 ndi Pemphelo
□ Phunzilo la Baibo la Mpingo:
bt mutu 15 ndime 8-12, ndi bokosi patsamba 118 (Mph. 30)
□ Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibo: Obadiya 1–Yona 4 (Mph. 10)
Na. 1: Yona 2:1-10 (Mph. 4 kapena zocepelapo)
Na. 2: Kodi Kulambila Koona Kumathandiza Bwanji Kuti Anthu Amitundu Yonse Akhale Ogwilizana?—Sal. 133:1 (Mph. 5)
Na. 3: N’cifukwa Ciani “Paladaiso” Wochulidwa pa Luka 23:43 Sangakhale Mbali Ina ya Hade Kapena ya Kumwamba?—rs tsa. 337 ndime 1-tsa. 338 ndime 1 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Nchito:
Nyimbo 95
Mph. 15: Kutumikila ku Malo Osoŵa Kumabweletsa Madalitso a Yehova. Kukambilana kozikidwa pa Nsanja ya Olonda ya October 15, 2012, masamba 3 mpaka 6. Pemphani omvela kuti akambepo zimene aphunzilapo.
Mph. 15: “Mungakwanitse—Musadzidelele.” Mafunso ndi mayankho. Funsani mwacidule munthu amene sanaphunzile kwambili, kapena wamanyazi koma amatsogoza maphunzilo a Baibo.
Nyimbo 26 ndi Pemphelo