Ndandanda ya Mlungu wa December 31
MLUNGU WA DECEMBER 31
Nyimbo 60 ndi Pemphelo
□ Phunzilo la Baibo la Mpingo:
bt mutu 17 ndime 1-7 (Mph. 30)
□ Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibo: Malaki 1-4 (Mph. 10)
Kubweleza za m’Sukulu ya Ulaliki (Mph. 20)
□ Msonkhano wa Nchito:
Nyimbo 72
Mph. 10: “Nkhani Yatsopano Imene Izipezeka mu Nsanja ya Olonda.” Nkhani. Gwilitsilani nchito ulaliki wacitsanzo umene uli patsamba 8, kuti muonetse mmene mungagwilitsilile nchito magazini poyambitsa phunzilo la Baibo pa Ciŵelu coyamba mu January.
Mph. 10: Kodi Tiphunzilapo Ciani? Kukambilana. Lemba la Luka 10:38-42 liŵelengedwe. Kambilanani mmene nkhani ili pa lembali ingatithandizile mu ulaliki.
Mph. 10: Cogaŵila ca mu January ndi February. Kukambilana. Kambilanani mfundo zina mu cofalitsa cimene tigaŵila, ndipo khalani ndi zitsanzo ziŵili.
Nyimbo 134 ndi Pemphelo