Ndandanda ya Mlungu wa September 30
MLUNGU WA SEPTEMBER 30
Nyimbo 99 ndi Pemphelo
□ Phunzilo la Baibo la Mpingo:
jl phunzilo 5 mpaka 7 (Mph. 30)
□ Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibo: Agalatiya 1-6 (Mph. 10)
Na. 1: Agalatiya 1:18–2:10 (Mph. 4 kapena zocepelapo)
Na. 2: N’cifukwa Ciani Pali Zipembedzo Zambili?—rs tsa. 83 ndime 1-tsa. 84 ndime 2 (Mph. 5)
Na. 3: N’cifukwa Ciani Yehova ali Woyenela Kulambilidwa?—Chiv. 4:11 (5 min.)
□ Msonkhano wa Nchito:
Nyimbo 108
Mph. 10: “Apempheni.” Kukambitsilana. Pambuyo pake, citani citsanzo ca mmene mungayambitsile phunzilo pa Ciŵelu coyamba m’October.
Mph. 10: Njila Zolalikilila Uthenga Wabwino—Kulalikila kwa Anthu a Zinenelo Zonse. Nkhani yokambitsilana yocokela m’buku la Gulu, tsamba104, ndime 2, mpaka tsamba 105, ndime 3. Khalani ndi citsanzo.
Mph. 10: Musade Nkhawa. (Mat. 6:31-33) Nkhani yokambitsilana yocokela mu Buku Lapachaka la 2013, tsamba 138, ndime 3, mpaka tsamba 139, ndime 3. Pemphani omvela kuti afotokoze maphunzilo amene apezapo.
Nyimbo 40 and Pemphelo