Ndandanda ya Mlungu wa September 29
MLUNGU WA SEPTEMBER 29
Nyimbo 69 ndi Pemphelo
Phunzilo la Baibulo la Mpingo:
jr mutu 14 ndime 8 mpaka 13 (Mph. 30)
Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibulo: Numeri 33–36 (Mph. 10)
Na. 1: Numeri 33:24-49 (Mph. 4 kapena zocepelapo)
Na. 2: Musadelele Mphamvu ya Mdyelekezi—rs tsa. 355 ndime 2-tsa. 356 ndime 1 (Mph. 5)
Na. 3: Khalani Osamala Munthu Wina Akakufunsani Cifukwa Cake Mumakhulupilila Zinthu Zinazake—bh tsa. 160 ndime 13-15 (Mph. 5)
Msonkhano wa Nchito:
Nyimbo 108
Mph. 10: Kuyambitsa Phunzilo la Baibulo pa Ciŵelu Coyamba. Nkhani yokambilana. Mwa kugwilitsila nchito ulaliki wa citsanzo umene uli pa tsamba 4, citani citsanzo ca mmene tingayambitsile phunzilo la Baibulo pa Ciŵelu coyamba mu October. Limbikitsani onse kutengako mbali.
Mph. 10: Kodi Tiphunzilapo Ciani? Nkhani yokambilana. Ŵelengani Machitidwe 4:13 ndi 2 Akorinto 4:1, 7. Kambilanani mmene Malembawa angatithandizile mu ulaliki.
Mph. 10: Funsani Mgwilizanitsi wa Bungwe la Akulu. Kodi mumagwila nchito yotani pa udindo wanu? Kodi mumaganizila ciani posankha abale okamba nkhani mu Msonkhano wa Nchito? N’cifukwa ciani sitiyenela kuona mgwilizanitsi wa bungwe la akulu kukhala wolamulila bungwe la akulu kapena mpingo?
Nyimbo 4 ndi Pemphelo