Ndandanda ya Mlungu wa January 19
MLUNGU WA JANUARY 19
Nyimbo 47 ndi Pemphelo
Phunzilo la Baibulo la Mpingo:
cl mutu 4 ndime 1 mpaka 9 (Mph. 30)
Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibulo: Oweruza 1-4 (Mph. 8)
Na. 1: Oweruza 3:1-11 (Mph. 3 kapena zocepelapo)
Na. 2: Mungaphunzile Bwanji za Mulungu?—igw-CIN tsa. 4 ndime 1-4 (Mph. 5)
Na. 3: Ahitofeli—Mutu: Yehova Amalepheletsa Ziwembu za Anthu Acinyengo—w12 4/15 tsa. 9 ndime 5 (Mph. 5)
Msonkhano wa Nchito:
Lemba la Mwezi: ‘Tumikilani Ambuye monga kapolo, modzicepetsa kwambili.’—Machitidwe 20:19.
Nyimbo 77
Mph. 10: Kodi Mukugwilitsila Nchito Zakumapeto za m’ Buku la Zimene Baibulo Imaphunzitsa M’ceni-ceni? Kukambitsilana kozikidwa pa mafunso otsatila: (1) Kodi Tingagwilitsile nchito bwanji zakumapeto kuthandiza amene timaphunzila nao Baibulo kumvetsa (a) Yesu Kristu—Mesiya Wolonjezedwa, ndi (b) Kodi Anthu Alidi ndi Mzimu Umene Sumafa? Pomaliza limbikitsani onse kugwilitsila nchito zakumapeto.
Mph. 10: Kutumikilani Ambuye Kumafuna Khama Ndiponso Kudzipeleka. Nkhani yokambilana yocokela mu Buku Lapacaka la Mboni za Yehova la 2014, tsa. 59, ndime 1, mpaka tsa. 62, ndime 1; ndi tsa. 67, ndime 2. Pemphani omvela kuti akambe zimene aphunzilapo.
Mph. 10: “Pitilizani Kupita Patsogolo Monga Mtumiki.” Mafunso ndi mayankho.
Nyimbo 20 ndi Pemphelo