Ndandanda ya Mlungu wa February 23
MLUNGU WA FEBRUARY 23
Nyimbo 21 ndi Pemphelo
Phunzilo la Baibulo la Mpingo:
cl mutu. 5 ndime 18-21 ndi bokosi tsa. 55 (Mph. 30)
Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibulo: Oweruza 19–21 (Mph. 8)
Kubweleza za M’sukulu ya Ulaliki (Mph. 20)
Msonkhano wa Nchito:
Lemba la Mwezi: Khalani “Odzipeleka pa Nchito Zabwino.”—Tito 2:14.
Nyimbo 75
Mph. 10: Zosowa za pampingo.
Mph. 10: Khalani Odzipeleka pa Kulambila Koona Monga Mmene Yesu Anacitila. Nkhani yocokela mu Nsanja ya Olonda ya May 15, 2013, tsamba 8, ndime 2, ndi Nsanja ya Olonda ya December 15, 2010, masamba 9-11, ndime 12-16. Gogomezelani mmene nchito yolalikila ilili yabwino ndiponso mwai kwa Akristu. (Tito 2:14) Fotokozani mmene kudziŵa coonadi kumatithandizila kulalikila uthenga wabwino ndi kucititsa maphunzilo a Baibulo modzipeleka. Yamikilani mpingo cifukwa ca kudzipeleka kumene wasonyeza pa nchito zabwino.
Mph. 10: “Lengezani Coonadi Conena za Yesu Modzipeleka.” Kukambilana. Wofalitsa acite “Citsanzo 1” cimene cili mu Nsanja ya Mlonda ya May 1, 2014 tsamba 10 ndime 8 ndipo wocita citsanzoyo afotokozenso fanizo lomwe lili pa tsamba 11 ndime 13.
Nyimbo 5 ndi Pemphelo