Ndandanda ya Mlungu wa March 16
MLUNGU WA MARCH 16
Nyimbo 65 ndi Pemphelo
Phunzilo la Baibulo la Mpingo:
cl mutu 6 ndime 16-21, bokosi pa tsa. 65 (Mph. 30)
Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibulo: 1 Samueli 5–9 (Mph. 8)
Na. 1: 1 Samueli 6:10-21 (Mph. 3 kapena zocepelapo)
Na. 2: Ataliya—Mutu: Pewani Mzimu Woipa Monga wa Yezebeli—w09 4/1 tsa. 24, 25 (Mph. 5)
Na. 3: Maulosi Amene Anakwanilitsidwa pa Yesu Monga Mesiya—igw-CIN tsa. 11 (Mph. 5)
Msonkhano wa Nchito:
Lemba la Mwezi: ‘Khalani Okonzeka Kugwila Nchito Iliyonse Yabwino.’—Tito 3:1.
Nyimbo 98
Mph. 10: Anadzipeleka Mofunitsitsa—Ku Taiwan. Kukambilana kozikidwa pa Nsanja ya Mlonda ya October 15, 2014 tsamba 3 mpaka 6. Kodi ofalitsa amene achulidwa m’nkhaniyi anakonzekela bwanji kupita ku dziko lina? Nanga apeza madalitso otani?
Mph. 20: “Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kupeza Anthu Owapelekela Magazini. Kukambilana. Mukamaliza kukambilana citani citsanzo cacidule coonetsa wofalitsa akuyambitsa phunzilo la Baibulo kwa munthu amene amamupelekela magazini. Ndiyeno funsani wofalitsa amene amapeleka magazini kwa munthu wina. Ndi anthu angati amene amapelekela magazini? Kodi amakonzekela bwanji ulendo ulionse? M’pempheni kuti afotokoze zocitika zosangalatsa.
Nyimbo 101 ndi Pemphelo