Ndandanda ya Mlungu wa April 6
MLUNGU WA APRIL 6
Nyimbo 124 ndi Pemphelo
Phunzilo la Baibulo la Mpingo
cl mutu 7 ndime18-22, bokosi pa tsa. 75 (Mph. 30)
Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibulo: 1 Samueli 16-18 (Mph. 8)
Na. 1: 1 Samueli 18:17-24 (Mph. 3 kapena zocepelapo)
Na. 2: Kodi Mulungu Ndiye Amacititsa Kuti Anthu Azivutika?—igw-CIN tsa.14 ndime 1-4 (Mph. 5)
Na. 3: Baraki—Mutu: Khalani Olimba Mtima Ndipo Musadzipezele Ulemelelo—w12 2/15 tsa. 12 ndime 9 (Mph. 5)
Msonkhano wa Nchito:
Lemba la Mwezi: ‘Khalani Okonzeka Kugwila Nchito Iliyonse Yabwino.’—Tito 3:1.
Nyimbo 85
Mph. 10: Kugaŵila Magazini mu April. Kukambilana. Yambani ndi citsanzo coonetsa mmene tingagaŵile magazini pogwilitsila nchito maulaliki acitsanzo. Kenako kambilanani maulaliki onse a citsanzo.
Mph. 10: Tinacita Zotani? Kukambilana. Pemphani omvela kuti akambe mapindu amene apeza pogwilitsila nchito mfundo za m’nkhani yakuti, “Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kupeza Anthu Owapelekela Magazini.” Ndiyeno afotokoze zocitika zabwino za mu ulaliki.
Mph. 10: Zosoŵa za pampingo.
Nyimbo 106 ndi Pemphelo