LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • km 3/15 tsa. 8
  • Zilengezo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Zilengezo
  • Utimiki Wathu wa Ufumu—2015
Utimiki Wathu wa Ufumu—2015
km 3/15 tsa. 8

Zilengezo

◼ March ndi April: Gaŵilani Nsanja ya Mlonda ndi Galamukani! May ndi June: Gaŵilani buku la Zimene Baibo Imaphunzitsa M’ceni-ceni, kapena kamodzi ka tumapepala twa uthenga utu: Kodi Baibo mumaiona bwanji?, Kodi zinthu zidzakhala bwanji mtsogolo? Kodi cofunika n’ciani kuti banja likhale la mtendele?, Kodi ndani maka-maka amene akulamulila dzikoli?, Kodi mavuto adzathadi? ndi kakuti Kodi n’zoona kuti akufa angakhalenso ndi moyo?

◼ Cikumbutso cidzakhalako pa Cisanu, pa April 3, 2015. Ngati mpingo wanu umasonkhana pa Cisanu, mungasankhe tsiku lina lililonse mlungu umenewo pamene ena sakugwilitsila nchito Nyumba ya Ufumu. Ngati simudzakhala ndi Msonkhano wa Nchito mlungu umenewo, mgwilizanitsi wa bungwe la akulu ayenela kusintha ndandanda kotelo kuti nkhani zofunika kwambili zidzakambidwe ku mpingo mwezi umenewo.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani