Ndandanda ya Mlungu wa November 9
MLUNGU WA NOVEMBER 9
Nyimbo 48 ndi Pemphelo
Phunzilo la Baibulo la Mpingo:
ia mutu 2 ndime 1-12 (Mph. 30)
Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibulo: 1 Mbiri 21-25 (Mph. 8)
Na. 1: 1 Mbiri 23:1-11 (Mph. 3 kapena zocepelapo)
Na. 2: Elisa—Mutu: Muzilemekeza Kwambili Atumiki a Yehova—w14 2/1 tsa. 28 ndime 3-tsa. 29 ndime 1 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Aramagedo N’ciani Makamaka? (Mph. 5)
Msonkhano wa Nchito:
Lemba la Mwezi: “Ineyo ndinabzala, Apolo anathilila, koma Mulungu ndiye anakulitsa.”—1 Akor. 3:6.
Nyimbo 98
Mph.10: “Ineyo Ndinabzala, Apolo Anathilila, Koma Mulungu Ndiye Anakulitsa.” Nkhani yozikidwa pa lemba la mwezi. (1 Akor. 3:6) Ngati nthawi ilipo, fotokozani mfundo za mu Nsanja ya Olonda ya March 1, 1993, masamba 20-23. Mwacidule chulani nkhani za mu Msonkhano wa Nchito za mwezi uno, ndipo fotokozani mmene zikugwilizanilana ndi lemba la mwezi.
Mph.20: “Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kugaŵila Buku la Zimene Baibo Imaphunzitsa.” Kukambilana. Citani zitsanzo ziŵili zacidule. Citsanzo coyamba, wofalitsa aseŵenzetse mfundo za m’nkhani ino, ndipo caciŵili wofalitsa agwilitsile nchito ulaliki umene amaona kuti ndi wogwila mtima.
Nyimbo 111 ndi Pemphelo