LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 March tsa. 2
  • March 7-13

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • March 7-13
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 March tsa. 2

March 7-13

ESITERE 6-10

  • Nyimbo 131 ndi Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Esitere Anaimila Yehova ndi Anthu Ake”: (Mph. 10)

    • Esitere 8:3, 4—Ngakhale kuti Esitere anali wotetezeka, iye anaika moyo wake pangozi cifukwa ca anthu ena (ia 143 ndime 24-25)

    • Esitere 8:5—Esitere anacita zinthu mwanzelu ndi Ahasiwero (w06–CN 3/1 11 ndime 8)

    • Esitere 8:17—Anthu ambili analoŵa Ciyuda (w06–CN 3/1 11 ndime 3)

  • Kufufuza Cuma Cakuuzimu: (Mph. 8)

    • Esitere 8:1, 2—Kodi ulosi umene Yakobo anakamba ali pafupi kufa wakuti Benjamini adzagaŵa zimene wafunkha madzulo, unakwanilitsidwa bwanji? (ia 142 pa kabokosi)

    • Esitere 9:10, 15, 16—Ngakhale kuti lamulo linalola kulanda zofunkha, n’cifukwa ciani Ayuda sanacite zimenezo? (w06–CN 3/1 11 ndime 4)

    • Kodi kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwandiphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ndi mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingagwilitsile nchito mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibulo: Esitere 8:1-9 (Mph. 4 kapena zocepelapo)

KUONJEZELA LUSO LANU MU ULALIKI

  • Konzekelani Maulaliki a Mwezi Uno (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani mavidiyo a maulaliki acitsanzo ndi kukambilana mfundo zake. Ngati n’zosatheka kuonelela mavidiyo, ofalitsa aluso acite zitsanzo. Kenako, kambilanani nkhani yakuti “Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Konzani Ulaliki Wanu Wogaŵila Magazini.”

UMOYO WATHU WACIKRISTU

  • Nyimbo 118

  • “Landilani Alendo”: (Mph. 15) Kukambilana. Pemphani omvela kuti afotokoze zocitika zosangalatsa zimene anapeza, cifukwa colandila alendo panthawi ya Cikumbutso caka catha. Citani citsanzo ca cocitika cimodzi cosangalatsa.

  • Phunzilo la Baibulo la Mpingo: ia mutu 10 ndime 12-21, ndi kubwelelamo pa tsa. 91 (Mph. 30)

  • Kubweleza Mfundo Zimene Taphunzila ndi Kufotokoza Zomwe Tidzaphunzila Mlungu Wotsatila (Mph. 3)

  • Nyimbo 69 ndi Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani