LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 May tsa. 6
  • May 23-29

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • May 23-29
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 May tsa. 6

May 23-29

SALIMO 19-25

  • Nyimbo 116 ndi Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Maulosi Amatiuza Zambili Zokhudza Mesiya”: (Mph. 10)

    • Sal 22:1—Mesiya anaoneka ngati wasiidwa ndi Mulungu (w11-CN 8/15 15 ndime 16)

    • Sal 22:7, 8—Mesiya adzanyozedwa (w11-CN 8/15 15 ndime 13)

    • Sal 22:18—Adzacita maele pazovala za Mesiya (w11-CN 8/15 15 ndime 14)

  • Kufufuza Cuma Cakuuzimu: (Mph. 8)

    • Sal 19:14—Kodi tingaphunzilepo ciani pa vesi limeneli? (w06-CN 5/15 19 ndime 8)

    • Sal 23:1, 2—Kodi Yehova ndi M’busa wabwino motani? (w02-CN 9/15 32 ndime 1-2)

    • Kodi kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwandiphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ndi mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingagwilitsile nchito mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibulo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Salimo 25:1-22

KUONJEZELA LUSO LANU MU ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) bh—Ŵelengani lemba pa cipangizo cokhala ndi intaneti.

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) bh—Seŵenzetsani JW Laibulale pofufuza, kuti mupeze vesi la m’Baibulo limene liyankha funso limene mwininyumba wafunsa.

  • Phunzilo la Baibulo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) bh 129-130 ndime 11-12—Citani citsanzo cacidule coonetsa wofalitsa akuonetsa wophunzila Baibulo mmene angagwilitsile nchito JW Laibulale pokonzekela phunzilo pa cipangizo cokhala ndi intaneti.

UMOYO WATHU WACIKRISTU

  • Nyimbo 55

  • “Mmene Tingaseŵenzetsele JW Laibulale”—Mbali 2: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani mavidiyo akuti Download and Manage Bibles ndi Search in a Bible or Publication ngati alipo. Ndiyeno kambilanani kamutu kothela pa nkhani imene mukukambilana. Pemphani omvela kuti akambe mmene anagwilitsila nchito JW Laibulale mu ulaliki.

  • Phunzilo la Baibulo la Mpingo: (Mph. 30) ia mutu 16 ndime 1-15

  • Kubweleza Mfundo Zimene Taphunzila ndi Kufotokoza Zomwe Tidzaphunzila Mlungu Wotsatila (Mph. 3)

  • Nyimbo 139 ndi Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani