May Umoyo ndi Utumiki Wathu Wacikristu—Kabuku ka Msonkhano May 2016 Maulaliki Acitsanzo May 2-8 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | YOBU 38-42 Yehova Amakondwela Tikamapemphelela Ena UMOYO WATHU WACIKRISTU Kodi Mukugwilitsila Nchito JW Laibulale? May 9-15 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | SALIMO 1-10 Kuti Tikhale Pamtendele ndi Yehova, Tifunika Kulemekeza Mwana Wake, Yesu May 16-22 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | SALIMO 11-18 Ndani Amene Angakhale Mlendo m’Cihema ca Yehova? UMOYO WATHU WACIKRISTU Mmene Tingaseŵenzetsele JW Laibulale May 23-29 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | SALIMO 19-25 Maulosi Amatiuza Zambili Zokhudza Mesiya May 30–June 5 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | SALIMO 26-33 Dalilani Yehova Kuti Akulimbitseni Mtima