LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 May tsa. 6
  • Maulosi Amatiuza Zambili Zokhudza Mesiya

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Maulosi Amatiuza Zambili Zokhudza Mesiya
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Nkhani Zofanana
  • Yesu Kristu—Mesiya Wolonjezedwa
    Zimene Baibo Imaphunzitsa M’ceni-ceni
  • Salimo 46:10—“Khalani Chete, Ndipo Dziŵani Kuti Ine Ndine Mulungu”
    Kufotokoza Mavesi a m’Baibulo
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 May tsa. 6

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | SALIMO 19-25

Maulosi Amatiuza Zambili Zokhudza Mesiya

LEMBA

ULOSI

KUKWANILITSIDWA KWAKE

Salimo 22:1

Anaoneka ngati wasiidwa ndi Mulungu

Mateyu 27:46; Maliko 15:34

Salimo 22:7, 8

Ananyozedwa ali pa mtengo wozunzikilapo

Mateyu 27:39-43

Salimo 22:16

Anakhomeleledwa ndi misomali pa mtengo wozunzikilapo

Mateyu 27:31; Maliko 15:25; Yohane 20:25

Salimo 22:18

Kucita maele pa zovala zake

Mateyu 27:35

Salimo 22:22

Amatsogolela panchito yodziŵitsa anthu za dzina la Yehova

Yohane 17:6

Munthu wotsutsa akumenya Yesu; pambuyo pake, anthu akulila pamene Yesu akufa pamtengo wozunzikilapo
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani