LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 July tsa. 8
  • Ndandanda ya Upainiya wa Nthawi Zonse

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Ndandanda ya Upainiya wa Nthawi Zonse
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 July tsa. 8

UMOYO WATHU WACIKHIRISTU

Ndandanda ya Upainiya wa Nthawi Zonse

Apainiya aŵili ali mu ulaliki

Upainiya wa nthawi zonse umafuna ndandanda yabwino. Ngati mumalalikila kwa maola 18 mlungu uliwonse, mukhoza kucita upainiya ndipo mungakhale ndi nthawi yocita zinthu zina. Ndandanda yotele, idzakuthandizani kukhala ndi nthawi yosamalila zakugwa mwadzidzidzi, monga matenda kapena nyengo ngati sili bwino. Pa chati cimene cili munsimu pali ndandanda zimene zingathandize amene amagwila nchito ya maola ocepa, amene amagwila nchito ya tsiku lonse, kapena amene ali ndi thanzi lofooka. Mukasintha zocita zina, wina m’banja angayambe kucita upainiya mu September. Bwanji osakambilana zimenezi pa kulambila kwanu kwa pa banja mlungu wotsatila?

NIMAGWILA NCHITO YA MAOLA OCEPA

Mande

NCHITO

Ciŵili

NCHITO

Citatu

NCHITO

Cinayi

Maola 6

Cisanu

Maola 6

Ciŵelu

Maola 4

Sondo

Maola 2

NIMAGWILA NCHITO YA TSIKU LONSE

Mande

Maola 2

Ciŵili

Maola 2

Citatu

MISONKHANO YA MKATI MWA MLUNGU

Cinayi

Maola 2

Cisanu

Maola 2

Ciŵelu

Maola 6

Sondo

Maola 4

NILI NDI THANZI LOFOOKA

Mande

KUPUMULA

Ciŵili

Maola 3

Citatu

Maola 3

Cinayi

Maola 3

Cisanu

Maola 3

Ciŵelu

Maola 3

Sondo

Maola 3

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani