LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 July tsa. 6
  • July 18-24

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • July 18-24
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 July tsa. 6

July 18-24

MASALIMO 74-78

  • Nyimbo 110 ndi Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Muziganizila Nchito za Yehova”: (Mph. 10)

    • Sal. 74:16; 77:6, 11, 12—Muziganizila mozama nchito za Yehova (w15 8/15, tsa. 10 ndime 3-4; w04 3/1-CN, masa. 19-20; w03 7/1-CN, tsa. 10 ndime 6-7)

    • Sal. 75:4-7—Nchito za Yehova ziphatikizapo kusankha amuna odzicepetsa kuti azisamalila mpingo (w06 7/15 -CN, tsa. 11 ndime 2; it-E 1, tsa. 1160 ndime 7)

    • Sal. 78:11-17—Ganizilani mmene Yehova anathandizila anthu ake (w04 4/1-CN, masa. 21-22)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 8)

    • Sal. 78:2—Kodi mau a vesi imeneyi anakwanilitsika bwanji pa Mesiya? (w11 8/15-CN, tsa. 11 ndime 14)

    • Sal. 78:40, 41—Malinga ni mavesi aya, kodi zocita zathu zingakhudze bwanji Yehova? (w12-CN 11/1, tsa. 14 ndime 5; w11-CN 7/1, tsa. 10)

    • Kodi kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ningaseŵenzetse mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibulo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Sal. 78:1-21

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) Nsanja ya Mlonda yogaŵila ya 2016 Na. 4 tsa. 16—Chulani za copeleka.

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Nsanja ya Mlonda yogaŵila ya 2016 Na. 4

  • Phunzilo la Baibulo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) Uthenga Wabwino phunzilo 5 ndime 6-7

UMOYO WATHU WACIKHIRISTU

  • Nyimbo 15

  • Zosoŵa za pa mpingo: (Mph. 10)

  • “Yehova Analenga Zinthu Zonse”: (Mph. 5)Kukambilana. Tambitsani vidiyo ya pa jw.org yakuti Yehova Analenga Zinthu Zonse”. (Pitani pa MABUKU > MAVIDIYO.) Pambuyo pake, pemphani ana amene asankhidwa kuti abwele kutsogolo. Ndiyeno, afunseni mafunso ogwilizana ndi vidiyo imeneyo.

  • Phunzilo la Baibulo la Mpingo: (Mph. 30) ia mutu. 20 ndime 1-13

  • Kubwelelamo ndi Kuchulako za Mlungu Wotsatila (Mph. 3)

  • Nyimbo 73 ndi Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani