LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 July tsa. 6
  • Muzikumbukila Nchito za Yehova

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Muzikumbukila Nchito za Yehova
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Nkhani Zofanana
  • Phunzilani Zambili za Yehova Poyang’ana Cilengedwe Cake
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
  • Dalilani Yehova Kuti Akulimbitseni Mtima
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • “Yehova Ndi Wamkulu ndi Woyenela Kutamandidwa Kwambili”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 July tsa. 6

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MASALIMO 74-78

Muzikumbukila Nchito za Yehova

Kuganizila zinthu zabwino zimene Yehova wacita n’kofunika

Mlongo asinkhasinkha zimene waŵelenga m’Baibulo

74:16; 77:6, 11, 12

  • Kusinkhasinkha kudzatithandiza kumvetsetsa zimene timaŵelenga m’Mau a Mulungu, ndi kuyamikila mocokela pansi pa mtima cakudya cauzimu

  • Kuganizila mozama za Yehova kudzatithandiza kukumbukila nchito zake zodabwitsa, ndi ciyembekezo cimene tili naco

Nchito za Yehova ziphatikizapo:

74:16, 17; 75:6, 7; 78:11-17

  • Cilengedwe

    Tikamaphunzila zambili zokhudza cilengedwe, timayamba kuopa kwambili Yehova

  • Amuna osankhidwa mu mpingo

    Tiyenela kukhala ogonjela kwa anthu amene Yehova wawasankha kuti atitsogolele

  • Pamene Mulungu anapulumutsa anthu

    Kukumbukila zocitika pamene Yehova anapulumutsa anthu ake, kumalimbitsa cikhulupililo cathu mwa iye kuti ndi wofunitsitsa kusamalila anthu ake

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani