LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 September tsa. 4
  • “Thandizo Langa Licokela kwa Yehova”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Thandizo Langa Licokela kwa Yehova”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Nkhani Zofanana
  • Kodi Mudziŵa?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2024
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 September tsa. 4

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MASALIMO 120-134

“Thandizo Langa Licokela kwa Yehova”

Masalimo 120 mpaka 134 amadziŵika kuti ndi nyimbo zokwelela kumzinda. Ambili amakhulupilila kuti nyimbozi zinali kuimbidwa mwacisangalalo ndi Aisraeli popita ku Yerusalemu kukacita zikondwelelo zapacaka. Mzinda wa Yerusalemu unali pa malo okwela ku mapili a Yuda.

Aisiraeli apita ku Yerusalemu kukalambila

Citetezo ca Yehova cafotokozedwa kuti cili ngati. . .

121:3-8

  • M’busa

    mbusa wogalamuka

  • Mtengo upanga mthunzi woteteza ku dzuwa

    mthunzi woteteza ku dzuwa

  • Asilikali

    msilikali wokhulupilika

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani