LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 November tsa. 6
  • “Kumbukila Mlengi Wako Wamkulu Masiku a Unyamata Wako”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Kumbukila Mlengi Wako Wamkulu Masiku a Unyamata Wako”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Nkhani Zofanana
  • Tumikilani Yehova Asanafike Masiku Oipa
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2014
  • Mafunso Ocokela kwa Oŵelenga
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2024
  • Anthu a Yehova ni Okangalika pa Kulambila Koona
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 November tsa. 6

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU MLALIKI 7–12

“Kumbukila Mlengi Wako Wamkulu Masiku a Unyamata Wako”

Kumbukilani Mlengi wanu Wamkulu mukali acicepele mwa kuseŵenzetsa maluso anu pom’tumikila

Mnyamata waimilila mowongoka ndipo wokalamba waimilila mothandizidwa na ndondo

12:1, 13

  • Acicepele ambili ali ndi thanzi ndi mphamvu cakuti angakwanitse kugwila nchito zovuta

  • Acicepele ayenela kuseŵenzetsa nthawi na mphamvu zawo potumikila Yehova pamene akalibe kufooka na ukalamba

Solomo anafotokoza mavuto a ukalamba mwandakatulo

12:2-7

  • Azimayi asonjelela pa windo

    Vesi 3: “Akazi oyang’ana pawindo azidzaona mdima”

    Kusayang’ana bwino

  • Azimayi ayimba

    Vesi 4: “Ana onse aakazi azidzaimba nyimbo ndi mau otsika”

    Kuvutika kumva

  • Zipatso

    Vesi 5: “Zakudya sizidzakoma”

    Kusamvela kukoma kwa cakudya

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani