CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MASALIMO 69-73
Anthu a Yehova ni Okangalika pa Kulambila Koona
Cangu cathu pa kulambila koona cizionekela
69:9
Davide anali wacangu potumikila Yehova umoyo wake wonse
Davide sanalole munthu aliyense kutsutsana ndi Yehova kapena kutonza dzina la Mulungu
Acikulile angathandize acicepele kukhala okangalika
71:17, 18
Wolemba salimo imeneyi amene mwina ndi Davide, anaonetsa kuti anali wofunitsitsa kulimbikitsa mbadwo wotsatila
Makolo ndi Akhiristu ofikapo mwauzimu angaphunzitse acicepele
Tikakhala acangu timauzako ena zimene Ufumu wa Mulungu udzacitila anthu
72:3, 12, 14, 16-19
Vesi 3—Anthu onse adzakhala pa mtendele
Vesi 12—Osauka adzalanditsidwa
Vesi 14—Ciwawa cidzatha
Vesi 16—Aliyense adzakhala ndi cakudya ca mwana alilenji