LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 November tsa. 7
  • Acicepele—Musazengeleze Kuloŵa pa ‘Khomo Lalikulu’

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Acicepele—Musazengeleze Kuloŵa pa ‘Khomo Lalikulu’
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Nkhani Zofanana
  • Khalani na Zolinga Zauzimu Kuti Mulemekeze Mlengi Wanu
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2004
  • Acicepele, Kodi Mumaika Zolinga Zauzimu Patsogolo?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2018
  • Njila Zowonjezela Utumiki Wanu
    Gulu Lokhazikitsidwa Kucita Cifunilo ca Yehova
  • Kucita Upainiya
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 November tsa. 7

UMOYO WATHU WACIKHIRISTU

Acicepele—Musazengeleze Kuloŵa pa ‘Khomo Lalikulu’

N’capafupi kuona ngati tidzakhalabe acicepele ndipo “masiku oipa” amene amabwela cifukwa ca ukalamba m’dziko la Satanali, sangatifikile. (Mlal. 12:1) Ngati ndinu wacicepele, kodi mukuzengeleza kuyambako mautumiki monga utumiki wa nthawi zonse poganiza kuti mukali na nthawi yambili?

Tonse ‘zinthu zosayembekezeleka zimatigwela.’ (Mlal. 9:11) “Simukudziŵa kuti moyo wanu udzakhala wotani mawa.” (Yak. 4:14) Conco, musazengeleze kuyambako mautumiki osiyana-siyana malinga ndi zolinga zanu zauzimu. Loŵani pa “khomo lalikulu la mwayi wautumiki” likali lotseguka. (1 Akor. 16:9) Mukacita zimenezo, simudzadandaula.

Zolinga zauzimu zimene mungakhale nazo:

  • Mlongo wacicepele alalikila m’cinenelo cina

    Kulalikila anthu okamba cinenelo cina

  • Abale na alongo acicepele acita upainiya

    Upainiya

  • Abale na alongo acicepele ali m’sukulu yophunzitsa utumiki

    Kuloŵa masukulu ophunzitsa atumiki a Mulungu

  • Abale na alongo acicepele agwila nchito yomanga

    Nchito ya zomanga-manga

  • M’bale wacicepele atumikila pa Beteli

    Kutumikila pa Bateli

  • M’bale wacicepele ali m’chito yadela

    Kuyang’anila dela

Zolinga zanga:

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani