LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 December tsa. 4
  • December 12-18

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • December 12-18
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 December tsa. 4

December 12-18

YESAYA 6-10

  • Nyimbo 116 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Ulosi wa Mesiya Umene Unakwanilitsika”: (Mph. 10)

    • Yes. 9:1, 2—Ulaliki wake wapoyela ku Galileya unanenedwelatu (w11 8/15 tsa. 10 ndime 13; ip-1 tsa. 124-126 ndime 13-17)

    • Yes. 9:6—Adzakhala na maudindo ambili osiyana-siyana (w14 2/15 tsa. 12 ndime 18; w07 5/15 tsa. 6)

    • Yes. 9:7—Ulamulilo wake udzabweletsa mtendele wa zoona na cilungamo (ip-1 tsa. 132 ndime 28-29)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 8)

    • Yes. 7:3, 4—N’cifukwa ciani Yehova anapulumutsa Mfumu yoipa Ahazi? (w06 12/1 tsa. 9 ndime 4)

    • Yes. 8:1-4—Ulosi umenewu unakwanilitsika bwanji? (it-1 1219; ip-1 tsa. 111-112 ndime 23-24)

    • Kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani ine za Yehova?

    • Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno zimene ine ningaseŵenzetse mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Yes. 7:1-17

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) g16.6 nkhani ya pacikuto

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) g16.6 nkhani ya pacikuto

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) lv 34 tsa. 18—Onetsani mmene tingam’fikile pamtima wophunzila.

UMOYO WATHU WACIKHIRISTU

  • Nyimbo 10

  • “Ine Ndilipo! Nditumizeni.” (Yes. 6:8) (Mph. 15) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Kukatumikila ku Malo Osoŵa. (Yendani ku mavidiyo pa MISONKHANO NA UTUMIKI WATHU).

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30.) kr nkhani. 5 ndime 10-17, na bokosi pa tsamba 53”

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Mlungu Wotsatila (Mph. 3)

  • Nyimbo 150 na Pemphelo

    Cikumbutso: Lizani nyimbo yonse kamodzi, ndiyeno mpingo uyimbile pamodzi nyimboyo.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani