LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb17 February tsa. 2
  • February 6-12

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • February 6-12
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
mwb17 February tsa. 2

February 6-12

YESAYA 47-51

  • Nyimbo 120 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 mineti kapena kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Kumvela Yehova Kumabweletsa Madalitso”: (10 min.)

    • Yes. 48:17—Kulambila koona n’kozikidwa pa kumvela malangizo a Mulungu (ip-2 131 pala. 18)

    • Yes. 48:18—Yehova amatikonda ndipo amafuna kuti tizikondwela na umoyo (ip-2 peji 131 pala. 19)

    • Yes. 48:19—Kumvela kumabweletsa madalitso osatha (ip-2 peji 132 pala. 20-21)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Yes. 49:6—Kodi Mesiya anakhala bwanji “kuwala kwa mitundu ya anthu,” ngakhale kuti utumiki wake padziko lapansi unalekezela kwa Aisiraeli okha? (w07 1/15 peji 9 pala. 8)

    • Yes. 50:1—N’cifukwa ninji Yehova anafunsa Aisiraeli kuti: “Cili kuti cikalata cothetsela ukwati wa mayi wanu yemwe ndinamuthamangitsa?” (it-1 peji 643 pala. 4-5)

    • Kodi ine pacanga, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwaniphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino zimene ine pacanga ningaseŵenzetse mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 mineti kapena kucepelapo) Yes. 51:12-23

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Konzekelani Maulaliki a Mwezi Uno: (15 min.) Kukambilana kozikidwa pa “Maulaliki a Citsanzo.” Tambitsani vidiyo yake iliyonse, kenako kambilanani zimene mwaphunzilapo.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 89

  • Zosoŵa za Pampingo: (7 min.) Mungasankhe kukambilana zimene tiphunzilapo m’nkhani yopezeka mu Buku Lapacaka la 2016 pa mapeji 144-145)

  • Khala Bwenzi la Yehova—Mvela Yehova: (8 min.) Kukambilana. Yambani mwa kutambitsa vidiyo yakuti Khala Bwenzi la Yehova—Mvela Yehova (Yendani ku mavidiyo pa ANA). Pambuyo pake, kambilanani mafunso aya: Kodi cifukwa cacikulu comvelela Yehova n’ciani? (Miy. 27:11) Ni njila zina ziti zimene ana angaonetsele kuti ni omvela kwa Yehova? Ni njila zina ziti zimene acikulile angaonetsele kuti ni omvela kwa Yehova?)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr nkhani 8 pala. 1-7, na bokosi papeji 79.

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 98 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani