LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb17 February tsa. 1
  • Maulaliki a Citsanzo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Maulaliki a Citsanzo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • GALAMUKANI!
  • PHUNZITSANI COONADI
  • MVETSELANI KWA MULUNGU
  • KONZANI ULALIKI WANU
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Maulaliki Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
mwb17 February tsa. 1
Mlongo wacitsikana akamba ese ya cilengedwe m’kilasi

Mlongo wacitsikana akamba ese (essay) mkilasi

Maulaliki a Citsanzo

GALAMUKANI!

Galamukani! No. 1 2017 | Teen Depression—Why? What Can Help?

Funso: Malipoti akuonetsa kuti ciŵelengelo ca acicepele amene akuvutika maganizo cikuwonjezeleka modetsa nkhawa. Muganiza n’ciani cingathetse vutoli?

Cogaŵila: Magaziniyi ionetsa zimene acicepele angacite kuti alimbane na vutoli, ndi mmene makolo awo angawathandizile.

PHUNZITSANI COONADI

Baibo yotsegula

Funso: N’ciani cingathandize kuti banja likhale la cimwemwe?

Lemba: Aef. 5:33

Mfundo ya Coonadi: Mabanja amalimba ngati okwatilanawo amakondana ndi kulemekezana.

MVETSELANI KWA MULUNGU

Mvetselani kwa Mulungu

Funso: Kodi mungakonde kukhala m’dziko looneka conco? [Muonetseni mapeji 2-3, ndipo yembekezani ayankhe]

Lemba: Yer. 29:11

Cogaŵila: Kabuku aka kaonetsa mmene tingamvetselele kwa Mulungu kuti tidzasangalale na umoyo wabwino umene iye akuganizila kudzatipatsa mtsogolo. [Kambilanani mapeji 4-5.]

KONZANI ULALIKI WANU

Funso:

Lemba:

Cogaŵila:

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani