LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 January tsa. 1
  • Maulaliki Acitsanzo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Maulaliki Acitsanzo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • NSANJA YA MLONDA
  • GALAMUKANI!
  • UTHENGA WABWINO WOCOKELA KWA MULUNGU
  • LEMBANI ULALIKI WANU
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Maulaliki Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 January tsa. 1
Alongo akulalikila pogwilitsila nchito kabuku ka Uthenga Wabwino ku Madagascar

Alongo akulalikila pogwilitsila nchito kabuku ka Uthenga Wabwino ku Madagascar

Maulaliki Acitsanzo

NSANJA YA MLONDA

Cikuto ca Magazini a Nsanja ya Mlonda ya January 2016 | Why Be Honest

Funso: Anthu ambili amaona kuti Baibulo ndi buku lofunika kwambili, koma amaganiza kuti n’zosatheka kulimvetsetsa. Kodi inu mumaliona bwanji Baibulo?

Lemba: Aroma 15:4

Kugaŵila cofalitsa: Magazini iyi ikufotokoza umboni woonetsa kuti n’zotheka kumvetsetsa Baibulo. Ikufotokozanso zimene zingatithandize kulimvetsetsa.

GALAMUKANI!

Kugaŵila cofalitsa: Ndakubweletselani Galamukani! ya mwezi uno.

Funso: Taonani funso ili patsamba 2 komanso zimene anthu ambili amayankha. Nanga inu muganiza bwanji?

Lemba: Miy. 24:10 Nkhani iyi ifotokoza mfundo zina zothandiza.

UTHENGA WABWINO WOCOKELA KWA MULUNGU

Cikuto ca kabuku ka Uthenga Wabwino Wocokela kwa Mulungu

Kugaŵila cofalitsa: Ndabwela kudzakuuzani za phunzilo laulele la Baibulo. Kabuku aka kangakuthandizeni kudziŵa pamene mungapeze mayankho a mafunso ofunika kwambili m’Baibulo lanu.

Funso: Kodi munaphunzilapo Baibulo? [Yembekezani yankho.] Lekani ndikuonetseni mmene timaphunzilila. [Kambilanani funso 1 m’phunzilo 2.]

Lemba: Chiv. 4:11

LEMBANI ULALIKI WANU

Onani maulaliki acitsanzo amene asonyezedwa kale kuti akuthandizeni kulemba ulaliki wanu.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani