LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 May tsa. 1
  • Maulaliki Acitsanzo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Maulaliki Acitsanzo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • NSANJA YA MLONDA
  • NSANJA YA MLONDA (tsamba lomaliza)
  • ZIMENE BAIBO IMAPHUNZITSA
  • LEMBANI ULALIKI WANU
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Maulaliki Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 May tsa. 1
Mwamuna ndi mkazi wake akuphunzila Baibulo pamodzi poseŵenzetsa tabuleti

Mwamuna ndi mkazi wake akuphunzila Baibulo pamodzi poseŵenzetsa tabuleti

Maulaliki Acitsanzo

NSANJA YA MLONDA

Nsanja ya Mlonda Na. 3 2016 | Munthu Amene Mumakonda Akamwalila

Funso: Kodi mukhulupilila kuti mau awa adzakwanilitsidwa?

Lemba: Chiv. 21:3, 4

Kugaŵila Cofalitsa: Nsanja ya Mlonda iyi ifotokoza mmene Mulungu adzakwanilitsila lonjezo limeneli ndi mmene mudzapindulila.

NSANJA YA MLONDA (tsamba lomaliza)

Funso: Ndifuna kukuonetsani funso ili. [Onetsani mwininyumba funso loyamba ndi mayankho amene ali patsamba 16 m’magazini iyi.] Kodi muganiza bwanji?

Lemba: Sal. 83:18

Kugaŵila Cofalitsa: Nkhani iyi ifotokoza zinthu zina zimene Baibulo limaphunzitsa zokhudza dzina la Mulungu

ZIMENE BAIBO IMAPHUNZITSA

Zimene Baibo Imaphunzitsa m’Ceniceni?

Funso: Anthu ena amaganiza kuti Mulungu ndiye akulamulila dzikoli. Koma kodi mudziŵa kuti Baibulo siliphunzitsa zimenezo?

Lemba: 1 Yoh. 5:19

Kugaŵila Cofalitsa: Bukuli lifotokoza bwino zimene Baibulo limaphunzitsa m’ceniceni pa nkhani iyi komanso nkhani zina zambili.

LEMBANI ULALIKI WANU

Onani maulaliki acitsanzo amene asonyezedwa kale kuti akuthandizeni kulemba ulaliki wanu

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani