Alalikila pa msika ku Sierra Leone
Maulaliki a Citsanzo
GALAMUKANI!
Funso: N’cifukwa ciani zinthu padziko zikuipila-ipila?
Lemba: Yer. 10:23
Cogaŵila: Magazini ino ifotokoza cifukwa cake pali anthu ambili amene amakhulupilila kuti zinthu zidzakhala bwino m’tsogolo.
GALAMUKANI!
Funso: Kodi Mulungu ali na dzina?
Lemba: Sal. 83:18
Cogaŵila: Nkhani iyi ikamba za tanthauzo la dzina la Mulungu na cifukwa cake tifunika kuliseŵenzetsa. [Muonetseni nkhani yakuti “Zimene Baibulo Limanena—Dzina la Mulungu.”]
PHUNZITSANI COONADI
Funso: Kodi imfa monga mdani wathu idzathadi?
Lemba: 1 Akor. 15:26
Coonadi: Yehova adzacotsapo imfa kothelatu.
KONZANI ULALIKI WANU
Funso:
Lemba:
Cogaŵila: