Alalikila mayi ndi mwana wake ku West Bengal m’dziko la India
Maulaliki a Citsanzo
NSANJA YA MLONDA
Funso: Aliyense amafuna citonthozo nthawi zina. Kodi n’kuti kumene tingacipeze?
Lemba: 2 Akor. 1:3, 4
Cogaŵila: Magazini iyi ya Nsanja ya Mlonda ifotokoza mmene Mulungu amatitonthozela.
NSANJA YA MLONDA (cikuto cothela)
Funso: Anthu ena amaganiza kuti Ufumu wa Mulungu ni mtima wa munthu. Ena amaganiza kuti ndi mtendele umene anthu adzabweletsa padziko lonse. Inu muganiza bwanji?
Lemba: Dan. 2:44
Cogaŵila: Baibulo imakamba kuti Ufumu wa Mulungu ndi boma lenileni. Nkhani iyi ifotokoza zinthu zina zambili zimene Baibulo imakamba ponena za Ufumu wa Mulungu.
PHUNZITSANI COONADI
Funso: Tidziŵa bwanji kuti Mulungu amatidela nkhawa?
Lemba: 1 Pet. 5:7
Mfundo ya Coonadi: Mulungu amafuna kuti tizipemphela kwa iye cifukwa amatidela nkhawa.
KONZANI ULALIKI WANU
Funso:
Lemba:
Cogaŵila: