LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb17 January tsa. 1
  • Maulaliki a Citsanzo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Maulaliki a Citsanzo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • NSANJA YA MLONDA
  • PHUNZITSANI COONADI
  • UTHENGA WABWINO WOCOKELA KWA MULUNGU
  • KONZANI ULALIKI WANU
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Maulaliki Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
mwb17 January tsa. 1
Mboni za Yehova zilalikila ku Ghana

Alalikila uthenga wabwino ku Ghana

Maulaliki a Citsanzo

NSANJA YA MLONDA

Nsanja ya Mlonda Na. 1 2017 | Mmene mungapindulile Poŵelenga Baibo

Funso: Anthu ena amaganiza kuti Baibo inasila nchito, koma ena amakhulupilila kuti ikali yothandiza maningi. Nanga imwe muganiza bwanji?

Lemba: 2 Tim. 3:16, 17

Cogaŵila: Nsanja ya Mlonda iyi ifotokoza malangizo othandiza opezeka m’Baibo. Ndipo ionetsa zimene mungacite kuti mupindule na zimene mumaŵelenga m’Baibo.

PHUNZITSANI COONADI

Baibo yotsegula

Funso: Kodi mapeto a dziko ali pafupi?

Lemba: Mat. 24:3, 7, 14

Mfundo ya Coonadi: Maulosi a m’Baibo aonetsa kuti tili m’masiku otsiliza. Koma umenewu ni uthenga wabwino—cifukwa ni umboni wakuti zinthu zabwino zili pafupi.

UTHENGA WABWINO WOCOKELA KWA MULUNGU

Kodi Moyo Unacita Kulengedwa?

Cogaŵila: Nabwela kudzakuuzani za phunzilo laulele la Baibo. Kabuku aka kangakuthandizeni kudziŵa pamene mungapeze mayankho pa mafunso ofunika kwambili m’Baibo yanu?

Funso: Kodi munaphunzilapo Baibo? Lekani nikuonetseni mmene timaphunzilila. [Kambilanani funso 1, m’phunzilo 2]

Lemba: Chiv. 4:11

KONZANI ULALIKI WANU

Funso:

Lemba:

Cogaŵila:

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani