LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb17 February tsa. 3
  • February 13-19

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • February 13-19
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
mwb17 February tsa. 3

February 13-19

YESAYA 52-57

  • Nyimbo 148 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 mineti kapena kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Khristu Anavutika Cifukwa ca Ife”: (10 min.)

    • Yes. 53:3-5—Iye ananyozewa, na kuphwanyiwa cifukwa ca zocimwa zathu (w09 1/15 peji 26 pala. 3-5)

    • Yes. 53:7, 8—Na mtima wonse, Khristu anapeleka moyo wake cifukwa ca ise (w09 1/15 peji 27 pala. 10)

    • Yes. 53:11, 12—Tikhoza kukhala olungama cifukwa iye anakhalabe wokhulupilika mpaka imfa (w09 1/15 peji 28 pala. 13)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Yes. 54:1—Kodi “mkazi wosabeleka” wochulidwa mu ulosi umenewu n’ndani? Nanga “ana” ake n’ndani? (w06 3/15 peji 11 pala. 2)

    • Yes. 57:15—Kodi Yehova “amakhala” na munthu “wopsinjika” ndi “wa mtima wodzicepetsa” m’lingalilo lanji? (w05 10/15 peji 26 pala. 3)

    • Kodi ine pacanga, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwaniphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino zimene ine pacanga ningaseŵenzetse mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 mineti kapena kucepelapo) Yes. 57:1-11

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 mineti kapena kucepelapo) Gaŵilani kabuku ka Mvetselani kwa Mulungu, nakuyala maziko a ulendo wobwelelako.

  • Ulendo Wobwelelako: (4 mineti kapena kucepelapo) Citani citsanzo coonetsa ulendo wobwelelako kwa munthu amene analandila kabuku ka Mvetselani. Kambilanani mapeji 2-3, ndiyeno yalani maziko a ulendo wina wobwelelako.

  • Phunzilo la Baibo: (6 mineti kapena kucepelapo) bh peji 14-15 pala. 16-17—Ngati n’zotheka, tate acititse phunzilo kwa mwana wake mwamuna kapena mkazi.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 110

  • “Thandizani Ana Anu Kukhala na Cikhulupililo Colimba mwa Mlengi Wawo”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani Vidiyo yakuti Zimene Acicepele Anzanu Amakamba—Kukhulupilila mwa Mulungu. (yendani ku mavidiyo pa ACICEPELE).

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr nkhani 8 pala. 8-13, na chati pa peji 83”

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 107 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani